1 Samueli 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Patapita nthawi, kunabwera anthu amene anauza Davide kuti: “Afilisiti akuthira nkhondo mzinda wa Keila,+ ndipo akufunkha zokolola zimene zili pamalo opunthira mbewu.”+ Yobu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi inuyo simwam’tchinga iyeyo?+ Mwatchingiranso nyumba yake ndi chilichonse chimene ali nacho. Mwadalitsa ntchito ya manja ake+ ndipo ziweto zake zachuluka kwambiri padziko lapansi. Miyambo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+
23 Patapita nthawi, kunabwera anthu amene anauza Davide kuti: “Afilisiti akuthira nkhondo mzinda wa Keila,+ ndipo akufunkha zokolola zimene zili pamalo opunthira mbewu.”+
10 Kodi inuyo simwam’tchinga iyeyo?+ Mwatchingiranso nyumba yake ndi chilichonse chimene ali nacho. Mwadalitsa ntchito ya manja ake+ ndipo ziweto zake zachuluka kwambiri padziko lapansi.
11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+