Yoswa 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akisa ali pabulu pa ulendo wopita kunyumba, anakakamiza Otiniyeli kuti apemphe malo kwa Kalebe bambo ake. Ndiyeno Akisa anawomba m’manja kuitana bambo ake, ndipo Kalebe atamva, anam’funsa kuti: “Ukufuna chiyani?”+ 2 Mafumu 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno mayiyo anakwera bulu wake wamkazi+ n’kuuza wantchito wake kuti: “Kwera bulu utsogole. Uzithamanga, usayende pang’onopang’ono chifukwa cha ine, pokhapokha ndikakuuza.”
18 Akisa ali pabulu pa ulendo wopita kunyumba, anakakamiza Otiniyeli kuti apemphe malo kwa Kalebe bambo ake. Ndiyeno Akisa anawomba m’manja kuitana bambo ake, ndipo Kalebe atamva, anam’funsa kuti: “Ukufuna chiyani?”+
24 Ndiyeno mayiyo anakwera bulu wake wamkazi+ n’kuuza wantchito wake kuti: “Kwera bulu utsogole. Uzithamanga, usayende pang’onopang’ono chifukwa cha ine, pokhapokha ndikakuuza.”