Ekisodo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Mose anatenga mkazi wake ndi ana ake ndi kuwakweza pabulu, ndi kuyamba ulendo wobwerera ku Iguputo. Komanso, Mose anatenga ndodo ya Mulungu woona m’dzanja lake.+ 1 Samueli 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno pamene Abigayeli anali kutsika phiri atakwera bulu,+ mwadzidzidzi, anaona Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye akubwera, ndipo iye anakumana nawo.
20 Kenako Mose anatenga mkazi wake ndi ana ake ndi kuwakweza pabulu, ndi kuyamba ulendo wobwerera ku Iguputo. Komanso, Mose anatenga ndodo ya Mulungu woona m’dzanja lake.+
20 Ndiyeno pamene Abigayeli anali kutsika phiri atakwera bulu,+ mwadzidzidzi, anaona Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye akubwera, ndipo iye anakumana nawo.