Deuteronomo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+ 1 Samueli 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi.
25 Yehova adzakuchititsani kuti mugonje pamaso pa adani anu.+ Pokamenyana nawo nkhondo mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa pamaso pawo mudzadutsa njira 7. Mudzakhala chinthu chonyansa kwa mafumu onse a dziko lapansi.+
6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi.