Numeri 33:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Zikadzatero, zimene ndinafuna kuchita kwa anthuwo ndidzachita kwa inu.’”+ Deuteronomo 28:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu amene sunawadziwe adzadya zipatso za m’dziko lako ndi mbewu zako zonse.+ Motero udzakhala wodyeredwa ndi woponderezedwa nthawi zonse.+ 1 Mbiri 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amuna onse a Isiraeli amene anali m’chigwa ataona kuti asilikaliwo athawa, komanso kuti Sauli ndi ana ake afa, anayamba kuchoka m’mizinda yawo ndi kuthawa.+ Kenako Afilisiti anabwera n’kuyamba kukhala m’mizindayo.
33 Anthu amene sunawadziwe adzadya zipatso za m’dziko lako ndi mbewu zako zonse.+ Motero udzakhala wodyeredwa ndi woponderezedwa nthawi zonse.+
7 Amuna onse a Isiraeli amene anali m’chigwa ataona kuti asilikaliwo athawa, komanso kuti Sauli ndi ana ake afa, anayamba kuchoka m’mizinda yawo ndi kuthawa.+ Kenako Afilisiti anabwera n’kuyamba kukhala m’mizindayo.