Genesis 35:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake Debora+ mlezi wa Rabeka anamwalira, ndipo anamuika ku Beteli m’munsi mwa phiri, pansi pa mtengo waukulu. Choncho mtengowo anautcha kuti Aloni-bakuti.* 2 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Davide anatumiza mithenga kwa amuna a ku Yabesi-giliyadi+ kuti akawauze kuti: “Yehova akudalitseni,+ chifukwa munasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mbuye wanu Sauli mwa kumuika m’manda.+
8 Pambuyo pake Debora+ mlezi wa Rabeka anamwalira, ndipo anamuika ku Beteli m’munsi mwa phiri, pansi pa mtengo waukulu. Choncho mtengowo anautcha kuti Aloni-bakuti.*
5 Choncho Davide anatumiza mithenga kwa amuna a ku Yabesi-giliyadi+ kuti akawauze kuti: “Yehova akudalitseni,+ chifukwa munasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mbuye wanu Sauli mwa kumuika m’manda.+