Ekisodo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+ Salimo 78:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Iwo sanakumbukire mmene anaikira zizindikiro zake mu Iguputo,+Ndi zozizwitsa zimene anachita m’dera la Zowani,+ Salimo 78:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+
5 Pamenepo Aiguputo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzatambasula dzanja langa ndi kukantha Iguputo.+ Motero ndidzatulutsa ana a Isiraeli m’dzikolo.”+
43 Iwo sanakumbukire mmene anaikira zizindikiro zake mu Iguputo,+Ndi zozizwitsa zimene anachita m’dera la Zowani,+ Salimo 78:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+
51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+