1 Samueli 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso, n’zosatheka kuti ineyo ndichimwire Yehova mwa kusiya kukupemphererani.+ Ndipo ndiyenera kukulangizani+ za njira yabwino+ ndi yolondola. Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
23 Komanso, n’zosatheka kuti ineyo ndichimwire Yehova mwa kusiya kukupemphererani.+ Ndipo ndiyenera kukulangizani+ za njira yabwino+ ndi yolondola.
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+