2 Mbiri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha+ ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.+ Nehemiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu. Yoweli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wanu wonse.+ Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokuwa.+
3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha+ ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.+
9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu.
12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wanu wonse.+ Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokuwa.+