Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mukangolowa mumzinda, mum’peza ndithu asanapite kukadya kumalo okwezeka. Anthu sangayambe kudya pokhapokha iye atafika, chifukwa ndiye amadalitsa nsembeyo.+ Kenako oitanidwa amadya. Choncho pitani chifukwa mum’peza posachedwapa.”

  • 1 Samueli 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pamenepo wophikayo anatenga mwendo wonse n’kuuika patsogolo pa Sauli. Atatero anati: “Nyama imene inasungidwa ija ndi imeneyi. Tenga, udye chifukwa anasungira iweyo kuti udzaidye pa nthawi ino pamodzi ndi oitanidwa.” Chotero Sauli anadya pamodzi ndi Samueli pa tsikulo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena