-
Oweruza 6:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiyeno Gidiyoni analowa m’nyumba ndi kuphika nyama ya mwana wa mbuzi.+ Anatenganso ufa wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi kupanga mikate yopanda chofufumitsa.+ Atatero, anatenga nyamayo ndi kuiika m’dengu, ndipo msuzi anauika mumphika. Kenako, anatenga zinthu zimenezi ndi kukamupatsa mngelo uja pansi pa mtengo waukulu uja.
-