-
Machitidwe 28:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Choncho, popeza anali kutsutsana okhaokha, anayamba kuchoka, koma Paulo ananenabe mawu amodzi awa:
“Mzimu woyera unanena zoona kwa makolo anu kudzera mwa Yesaya mneneri.
-