1 Samueli 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo mzimu+ wa Yehova uyamba kugwira ntchito pa iwe, moti iweyo uyamba kulankhula monga mneneri+ pamodzi ndi aneneriwo, ndiponso usinthika kukhala wina. 1 Samueli 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo anapitiriza ulendo wake wopita ku Nayoti, ku Rama, ndipo mzimu+ wa Mulungu unafika ngakhalenso pa iye. Zitatero, iye anapitiriza kuyenda ndi kuchita zinthu ngati mneneri mpaka kukafika ku Nayoti, ku Rama.
6 Pamenepo mzimu+ wa Yehova uyamba kugwira ntchito pa iwe, moti iweyo uyamba kulankhula monga mneneri+ pamodzi ndi aneneriwo, ndiponso usinthika kukhala wina.
23 Pamenepo anapitiriza ulendo wake wopita ku Nayoti, ku Rama, ndipo mzimu+ wa Mulungu unafika ngakhalenso pa iye. Zitatero, iye anapitiriza kuyenda ndi kuchita zinthu ngati mneneri mpaka kukafika ku Nayoti, ku Rama.