Yoswa 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ ulula kwa iye.+ Tandiuza+ chonde, n’chiyani chimene wachita? Usandibisire.”+ Aroma 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero aliyense wa ife adzayankha yekha kwa Mulungu.+
19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ ulula kwa iye.+ Tandiuza+ chonde, n’chiyani chimene wachita? Usandibisire.”+