1 Samueli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo. 1 Samueli 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Thanthwe limodzi looneka ngati dzinolo linali kumpoto ndipo linaima ngati chipilala moyang’ana ku Mikimasi,+ ndipo linalo linali kum’mwera moyang’ana ku Geba.+ Yesaya 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye waukira Ayati.+ Wadutsa ku Migironi. Waika katundu wake ku Mikimasi.+
2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo.
5 Thanthwe limodzi looneka ngati dzinolo linali kumpoto ndipo linaima ngati chipilala moyang’ana ku Mikimasi,+ ndipo linalo linali kum’mwera moyang’ana ku Geba.+