1 Samueli 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye anatenga onsewo+ ndi kupita nawo ku Bezeki. Ana a Isiraeli analipo 300,000, ndipo amuna a ku Yuda analipo 30,000. 1 Samueli 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Samueli ananyamuka kuchoka ku Giligala kupita ku Gibeya wa ku Benjamini. Ndiyeno Sauli anayamba kuwerenga anthu amene anali nayebe limodzi, ndipo anapeza amuna pafupifupi 600.+
8 Ndiye anatenga onsewo+ ndi kupita nawo ku Bezeki. Ana a Isiraeli analipo 300,000, ndipo amuna a ku Yuda analipo 30,000.
15 Kenako Samueli ananyamuka kuchoka ku Giligala kupita ku Gibeya wa ku Benjamini. Ndiyeno Sauli anayamba kuwerenga anthu amene anali nayebe limodzi, ndipo anapeza amuna pafupifupi 600.+