Mlaliki 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Samala mayendedwe+ ako ukapita kunyumba ya Mulungu woona. Ukapita kumeneko uzikamvetsera,+ osati uzikapereka nsembe monga mmene amachitira anthu opusa,+ pakuti iwo sadziwa kuti akuchita zoipa.+
5 Samala mayendedwe+ ako ukapita kunyumba ya Mulungu woona. Ukapita kumeneko uzikamvetsera,+ osati uzikapereka nsembe monga mmene amachitira anthu opusa,+ pakuti iwo sadziwa kuti akuchita zoipa.+