Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 ndinaganiza+ kuti, ‘Tsopano Afilisitiwa abwera ku Giligala kuno kudzamenyana nane, ndipo sindinakhazike pansi mtima wa Yehova kuti atikomere mtima.’ Choncho ndakakamizika+ kupereka nsembe yopsereza.”

  • 1 Samueli 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo.

  • Miyambo 21:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Nsembe ya anthu oipa ndi yonyansa.+ Ndiye kuli bwanji munthu akaiperekera limodzi ndi makhalidwe otayirira?+

  • Yesaya 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Musabweretsenso nsembe zina zaufa zopanda phindu.+ Zofukiza zanu ndikunyansidwa nazo.+ Mumasunga masiku okhala mwezi+ ndi sabata,+ ndipo mumaitanitsa misonkhano.+ Koma ine ndatopa kukuonani mukugwiritsira ntchito mphamvu zamatsenga+ pamene mukuchita misonkhano yapadera.

  • Hoseya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena