1 Samueli 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki+ ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani uli wekha popanda munthu wina?”+ Luka 8:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Choncho khamu lonse lochokera m’midzi yapafupi ya Agerasa linam’pempha kuti achoke kwawoko, chifukwa linagwidwa ndi mantha aakulu.+ Pamenepo iye anakwera ngalawa kuti azipita.
21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki+ ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani uli wekha popanda munthu wina?”+
37 Choncho khamu lonse lochokera m’midzi yapafupi ya Agerasa linam’pempha kuti achoke kwawoko, chifukwa linagwidwa ndi mantha aakulu.+ Pamenepo iye anakwera ngalawa kuti azipita.