2 Samueli 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako mfumu inauza Ziba kuti: “Taona, zonse zimene zinali za Mefiboseti+ ndi zako.” Pamenepo Ziba anati: “Ndikuwerama+ pamaso panu. Pitirizani kundikomera mtima mbuyanga mfumu.” Miyambo 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+ Miyambo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+
4 Kenako mfumu inauza Ziba kuti: “Taona, zonse zimene zinali za Mefiboseti+ ndi zako.” Pamenepo Ziba anati: “Ndikuwerama+ pamaso panu. Pitirizani kundikomera mtima mbuyanga mfumu.”
17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+
4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+