2 Samueli 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma mfumu inayankha Abisalomu kuti: “Ayi mwana wanga. Tisachite kupita tonse, chifukwa tingakhale mtolo wolemetsa kwa iwe.” Ngakhale kuti Abisalomu anachondererabe,+ mfumu sinalole kupita koma inamudalitsa.+ 2 Samueli 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo Davide anamuuza kuti: “Ukapita nane limodzi, ukhala mtolo wolemetsa kwa ine.+
25 Koma mfumu inayankha Abisalomu kuti: “Ayi mwana wanga. Tisachite kupita tonse, chifukwa tingakhale mtolo wolemetsa kwa iwe.” Ngakhale kuti Abisalomu anachondererabe,+ mfumu sinalole kupita koma inamudalitsa.+