35 Ine lero ndili ndi zaka 80.+ Kodi ine mtumiki wanu ndingasiyanitse chabwino ndi choipa kapena kumva kukoma kwa zimene ndadya ndi kumwa?+ Kodi ine ndingathenso kumva+ mawu a amuna ndi akazi oimba?+ Ndiye ine mtumiki wanu ndikhalirenji mtolo wolemetsa+ kwa inu mbuyanga mfumu?