Ezara 2:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 kupatulapo akapolo awo aamuna ndi akapolo awo aakazi amene analipo 7,337. Iwo analinso ndi oimba aamuna+ ndi aakazi 200. Nehemiya 7:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 kupatulapo akapolo awo aamuna+ ndi akapolo awo aakazi amene analipo 7,337.+ Iwo analinso ndi oimba aamuna+ ndi aakazi+ 245. Mlaliki 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndinapezanso siliva ndi golide wambiri,+ ndi chuma chimene chimakhala ndi mafumu ndiponso chimene chimapezeka m’zigawo za dziko.+ Ndinali ndi oimba aamuna ndi aakazi.+ Ndinalinso ndi akazi ambiri,+ omwe amasangalatsa mtima+ wa amuna.
65 kupatulapo akapolo awo aamuna ndi akapolo awo aakazi amene analipo 7,337. Iwo analinso ndi oimba aamuna+ ndi aakazi 200.
67 kupatulapo akapolo awo aamuna+ ndi akapolo awo aakazi amene analipo 7,337.+ Iwo analinso ndi oimba aamuna+ ndi aakazi+ 245.
8 Ndinapezanso siliva ndi golide wambiri,+ ndi chuma chimene chimakhala ndi mafumu ndiponso chimene chimapezeka m’zigawo za dziko.+ Ndinali ndi oimba aamuna ndi aakazi.+ Ndinalinso ndi akazi ambiri,+ omwe amasangalatsa mtima+ wa amuna.