Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndipo pamene amuna anali kuimba, Miriamu anathirira mang’ombe kuti:+

      “Imbirani Yehova+ pakuti wakwezeka koposa.+

      Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.”+

  • 1 Samueli 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, pamene asilikali anali kubwerera, Davide atakantha Mfilisiti uja, akazi anayamba kutuluka m’mizinda yonse ya Isiraeli akuimba nyimbo+ ndi kuvina. Iwo anali kupita kukachingamira mfumu Sauli mosangalala,+ akuimba maseche+ komanso choimbira cha zingwe zitatu.

  • 2 Samueli 19:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ine lero ndili ndi zaka 80.+ Kodi ine mtumiki wanu ndingasiyanitse chabwino ndi choipa kapena kumva kukoma kwa zimene ndadya ndi kumwa?+ Kodi ine ndingathenso kumva+ mawu a amuna ndi akazi oimba?+ Ndiye ine mtumiki wanu ndikhalirenji mtolo wolemetsa+ kwa inu mbuyanga mfumu?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena