1 Mbiri 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sibekai+ Mhusati, Ilai Muahohi,+ 1 Mbiri 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno nkhondo imeneyi itatha, panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti+ ku Gezeri.+ Pa nthawi imeneyo Sibekai+ Mhusati anapha Sipa, amene anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai,+ moti Afilisiti anagonjetsedwa. 1 Mbiri 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mtsogoleri wa 8, wa mwezi wa 8, anali Sibekai+ Mhusati, wochokera mwa Azera.+ Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
4 Ndiyeno nkhondo imeneyi itatha, panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti+ ku Gezeri.+ Pa nthawi imeneyo Sibekai+ Mhusati anapha Sipa, amene anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai,+ moti Afilisiti anagonjetsedwa.
11 Mtsogoleri wa 8, wa mwezi wa 8, anali Sibekai+ Mhusati, wochokera mwa Azera.+ Gulu lake linali ndi anthu 24,000.