2 Samueli 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno pambuyo pa nkhondo imeneyi panabukanso nkhondo ndi Afilisiti ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ Mhusati+ anapha Safi, amene anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai.+
18 Ndiyeno pambuyo pa nkhondo imeneyi panabukanso nkhondo ndi Afilisiti ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ Mhusati+ anapha Safi, amene anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai.+