2 Samueli 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno pambuyo pa nkhondo imeneyi panabukanso nkhondo ndi Afilisiti ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ Mhusati+ anapha Safi, amene anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai.+ 1 Mbiri 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mtsogoleri wa 8, wa mwezi wa 8, anali Sibekai+ Mhusati, wochokera mwa Azera.+ Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
18 Ndiyeno pambuyo pa nkhondo imeneyi panabukanso nkhondo ndi Afilisiti ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ Mhusati+ anapha Safi, amene anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai.+
11 Mtsogoleri wa 8, wa mwezi wa 8, anali Sibekai+ Mhusati, wochokera mwa Azera.+ Gulu lake linali ndi anthu 24,000.