Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako Sauli anatumiza amithenga+ kunyumba ya Davide kuti akaizungulire ndi kupha Davide m’mawa mwa tsiku limenelo.+ Koma Mikala mkazi wa Davide anauza Davideyo kuti: “Ngati supulumutsa moyo wako usiku uno, mawa ukhala utaphedwa.”

  • 1 Samueli 23:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako Sauli anakhala mbali imodzi ya phiri ndipo Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anali mbali inanso ya phirilo. Zitatero Davide ananyamuka mofulumira kuti athawe+ Sauli. Pa nthawiyi n’kuti Sauli ndi asilikali ake atatsala pang’ono kupeza ndi kugwira Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye.+

  • 2 Samueli 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Abisalomu anatumiza akazitape+ m’mafuko onse a Isiraeli ndipo anawauza kuti: “Mukangomva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, munene kuti, ‘Abisalomu wakhala mfumu+ ku Heburoni!’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena