Salimo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adaniwo anandifikira m’tsiku la tsoka langa,+Koma Yehova anandichirikiza.+ Salimo 118:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mitundu yonse ya anthu inandizungulira,+Koma ndinali kuikankhira kutali m’dzina la Yehova.+ Yesaya 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndani pakati panu amene amaopa+ Yehova ndi kumvera mawu a mtumiki wake?+ Ndani amayenda mu mdima wokhawokha+ ndipo alibe kuwala? Iye akhulupirire dzina la Yehova+ ndipo adalire Mulungu wake.+
10 Ndani pakati panu amene amaopa+ Yehova ndi kumvera mawu a mtumiki wake?+ Ndani amayenda mu mdima wokhawokha+ ndipo alibe kuwala? Iye akhulupirire dzina la Yehova+ ndipo adalire Mulungu wake.+