Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano munthu woopa Yehova ndani?+

      Adzamulangiza kuyenda m’njira imene adzasankha.+

  • Salimo 112:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 112 Tamandani Ya, anthu inu!+

      א [ʼAʹleph]

      Wodala ndi munthu woopa Yehova,+

      ב [Behth]

      Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+

  • Mlaliki 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.

  • Malaki 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pa nthawi imeneyo anthu oopa Yehova+ analankhulana, aliyense ndi mnzake, ndipo Yehova anatchera khutu ndi kumvetsera.+ Buku la chikumbutso linayamba kulembedwa pamaso pake.+ Buku limeneli linali lonena za anthu oopa Yehova ndi anthu amene anali kuganizira za dzina lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena