Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 29:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pamene anachititsa nyale yake kuwala pamutu panga,

      Pamene ndinkayenda mu mdima iye akundiunikira ndi kuwala kwake.+

  • Salimo 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ngakhale ndikuyenda m’chigwa cha mdima wandiweyani,+

      Sindikuopa kanthu,+

      Pakuti inu muli ndi ine.+

      Chibonga chanu ndi ndodo yanu ndi zimene zimandilimbikitsa.+

  • Yesaya 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu amene anali kuyenda mu mdima, aona kuwala kwakukulu.+ Anthu amene anali kukhala m’dziko la mdima wandiweyani,+ kuwala kwawawalira.+

  • Yesaya 59:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 N’chifukwa chake chilungamo chatitalikira kwambiri, ndipo zolungama sizikutipeza. Tinali kuyembekezera kuunika koma m’malomwake tikungoona mdima. Tinali kuyembekezera kuwala koma tikungoyendabe mu mdima wosatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena