-
1 Mbiri 21:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kuwonjezera pamenepo, Mulungu woona anatumiza mngelo ku Yerusalemu kuti akawononge mzindawo.+ Mngeloyo atangoyamba kuwononga, Yehova anaona zimenezo ndi kumva chisoni chifukwa cha tsokalo,+ choncho anauza mngelo amene anali kuwonongayo kuti: “Basi pakwanira!+ Tsitsa dzanja lako tsopano.” Pa nthawiyi, mngelo wa Yehova uja anali ataimirira pafupi ndi malo opunthira mbewu a Orinani+ Myebusi.+
-