Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. Ekisodo 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Amene wamenya munthu mpaka munthuyo kufa ayenera kuphedwa ndithu.+ Numeri 35:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo, mnzakeyo n’kufa, ameneyo ndi wakupha munthu.+ Ndipo wakupha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+ Numeri 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Aliyense wopezeka kuti wapha munthu,+ atatsimikiziridwa ndi mboni,+ aphedwe. Koma umboni wa munthu mmodzi si wokwanira kuti munthu aphedwe.
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.
16 “‘Ngati munthu wamenya mnzake ndi chitsulo, mnzakeyo n’kufa, ameneyo ndi wakupha munthu.+ Ndipo wakupha munthuyo ayenera kuphedwa ndithu.+
30 “‘Aliyense wopezeka kuti wapha munthu,+ atatsimikiziridwa ndi mboni,+ aphedwe. Koma umboni wa munthu mmodzi si wokwanira kuti munthu aphedwe.