14 Likasa la Mulungu woona linakhalabe ndi banja la Obedi-edomu kunyumba kwake+ kwa miyezi itatu, ndipo Yehova anapitiriza kudalitsa+ banja la Obedi-edomu, ndi zinthu zake zonse.
25 Koma Davide+ ndi akulu a Isiraeli+ ndiponso atsogoleri+a anthu 1,000 aliyense, anali kuyenda mosangalala+ kupita kunyumba kwa Obedi-edomu,+ kukatenga likasa la pangano la Yehova.