1 Mbiri 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Davide atangoyamba kukhala m’nyumba yake,+ anauza Natani+ mneneri kuti: “Ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ koma likasa+ la pangano la Yehova likukhala m’chihema chansalu.”+
17 Ndiyeno Davide atangoyamba kukhala m’nyumba yake,+ anauza Natani+ mneneri kuti: “Ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ koma likasa+ la pangano la Yehova likukhala m’chihema chansalu.”+