1 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya. 1 Mbiri 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zokhudza Davide mfumu, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa pakati pa mawu a Samueli wamasomphenya,*+ Natani+ mneneri, ndiponso pakati pa mawu a Gadi+ wamasomphenya.
8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya.
29 Nkhani zokhudza Davide mfumu, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa pakati pa mawu a Samueli wamasomphenya,*+ Natani+ mneneri, ndiponso pakati pa mawu a Gadi+ wamasomphenya.