2 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+ 1 Mbiri 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kumanga nyumba+ zake mu Mzinda wa Davide, ndipo anakonza malo+ oikapo likasa la Mulungu woona, n’kulimangira hema. 2 Mbiri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Davide anali atachotsa likasa+ la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu+ n’kukaliika kumalo amene iye anakonza,+ pakuti anali atamanga hema wa likasalo ku Yerusalemu.+
2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+
15 Davide anapitiriza kumanga nyumba+ zake mu Mzinda wa Davide, ndipo anakonza malo+ oikapo likasa la Mulungu woona, n’kulimangira hema.
4 Koma Davide anali atachotsa likasa+ la Mulungu woona ku Kiriyati-yearimu+ n’kukaliika kumalo amene iye anakonza,+ pakuti anali atamanga hema wa likasalo ku Yerusalemu.+