Levitiko 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzakupatsani mtendere m’dzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsani.+ M’dziko lanu simudzapezeka zilombo zoopsa zakutchire,+ ndipo simudzadutsa lupanga.+ 1 Mafumu 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano Yehova Mulungu wanga wandipatsa mpumulo pakati pa adani anga onse ondizungulira.+ Palibe amene akulimbana nane, ndipo palibe choipa chilichonse chimene chikuchitika.+
6 Ndidzakupatsani mtendere m’dzikolo,+ moti mudzagona pansi popanda wokuopsani.+ M’dziko lanu simudzapezeka zilombo zoopsa zakutchire,+ ndipo simudzadutsa lupanga.+
4 Tsopano Yehova Mulungu wanga wandipatsa mpumulo pakati pa adani anga onse ondizungulira.+ Palibe amene akulimbana nane, ndipo palibe choipa chilichonse chimene chikuchitika.+