Salimo 89:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+ Salimo 132:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana ako akadzasunga pangano langa+Ndi zikumbutso zanga zimene ndidzawapatsa,+Ngakhalenso ana awo+Adzakhala pampando wako wachifumu kwamuyaya.”+
36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+
12 Ana ako akadzasunga pangano langa+Ndi zikumbutso zanga zimene ndidzawapatsa,+Ngakhalenso ana awo+Adzakhala pampando wako wachifumu kwamuyaya.”+