2 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho akulu onse+ a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni, ndipo Mfumu Davide anachita nawo pangano+ ku Heburoni pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza+ Davide kukhala mfumu ya Isiraeli.+ 2 Samueli 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Heburoni analamulira monga mfumu ya Yuda zaka 7 ndi miyezi 6.+ Ku Yerusalemu+ analamulira monga mfumu ya Isiraeli yense ndiponso Yuda zaka 33.
3 Choncho akulu onse+ a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni, ndipo Mfumu Davide anachita nawo pangano+ ku Heburoni pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza+ Davide kukhala mfumu ya Isiraeli.+
5 Ku Heburoni analamulira monga mfumu ya Yuda zaka 7 ndi miyezi 6.+ Ku Yerusalemu+ analamulira monga mfumu ya Isiraeli yense ndiponso Yuda zaka 33.