Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 20:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pambuyo pake mneneri uja+ anapita kwa mfumu ya Isiraeli n’kuiuza kuti: “Pitani, kalimbitseni gulu lanu lankhondo+ ndi kuganizira zomwe mudzachite,+ popeza kumayambiriro kwa chaka chamawa mfumu ya Siriya ija idzabweranso kudzamenyana nanu.”+

  • 2 Mbiri 36:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kumayambiriro+ kwa chaka, Mfumu Nebukadinezara inatuma+ asilikali ake omwe anakamutenga n’kubwera naye ku Babulo+ limodzi ndi zinthu zabwinozabwino za m’nyumba ya Yehova.+ Kuwonjezera apo, Nebukadinezara analonga ufumu Zedekiya+ yemwe anali m’bale wa bambo ake kukhala mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena