2 Pamene analemba kalata imeneyi, mfumu Yekoniya,+ mayi a mfumu,+ nduna za panyumba ya mfumu, akalonga a Yuda ndi Yerusalemu,+ amisiri ndi omanga makoma achitetezo+ anali atatengedwa kupita ku ukapolo kuchokera ku Yerusalemu.
9 Kenako anaukola ndi ngowe n’kuuika m’kakhola ndi kupita nawo kwa mfumu ya Babulo.+ Anapita nawo ataukulunga ndi ukonde wosakira kuti mawu ake asamvekenso m’mapiri a ku Isiraeli.+