9 Yehoyakini+ anali ndi zaka 18 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu+ ndi masiku 10 ku Yerusalemu. Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+
20 zimene Nebukadinezara mfumu ya Babulo anasiya pamene anatenga Yekoniya+ mwana wa Yehoyakimu, mfumu ya Yuda, pamodzi ndi olemekezeka onse a Yuda ndi Yerusalemu, kupita nawo ku ukapolo ku Babulo kuchokera ku Yerusalemu.+
4 “‘Ndipo Yekoniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, ndiponso anthu onse a mu Yuda amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo+ ndiwabwezeretsa kuno, pakuti ndithyola goli+ la mfumu ya Babulo,’ watero Yehova.”