Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mfumuyo inatenga+ anthu onse a ku Yerusalemu, akalonga onse,+ amuna onse amphamvu ndi olimba mtima,+ mmisiri aliyense+ ndi munthu aliyense womanga makoma achitetezo, n’kupita nawo ku Babulo. Anthu onse amene inawatenga analipo 10,000. Palibe amene anatsala, kupatulapo anthu onyozeka+ okha a m’dzikolo.

  • Yeremiya 24:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiyeno Yehova anandisonyeza madengu awiri a nkhuyu amene anali patsogolo pa kachisi wa Yehova. Anandisonyeza zimenezi Nebukadirezara mfumu ya Babulo atatenga Yekoniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, pamodzi ndi akalonga a Yuda, amisiri+ ndi omanga makoma achitetezo kuchokera ku Yerusalemu kupita nawo ku ukapolo ku Babulo.+

  • Yeremiya 29:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Awa ndi mawu a m’kalata imene mneneri Yeremiya anatumiza kuchokera ku Yerusalemu kupita kwa akuluakulu otsala pakati pa anthu amene anali ku ukapolo, kwa ansembe ndi kwa aneneri. Kalatayi inapitanso kwa anthu onse amene Nebukadinezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ku Babulo kuchokera ku Yerusalemu.+

  • Danieli 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno mfumu inauza Asipenazi, mkulu wa nduna za panyumba ya mfumu+ kuti abweretse ena mwa ana a Isiraeli, ana a m’banja lachifumu, ndi ana a anthu olemekezeka,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena