Esitere 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Moredekai anali atatengedwa ku Yerusalemu pamodzi ndi anthu amene anatengedwa kupita ku ukapolo.+ Anthuwa ndi amene anatengedwa pamodzi ndi Yekoniya+ mfumu ya Yuda, amene Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anam’tenga kupita naye ku ukapolo. Ezekieli 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa tsiku lachisanu la mweziwo, m’chaka chachisanu kuchokera pamene Mfumu Yehoyakini anatengedwa ukapolo,+ Danieli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakati pa anawo panali ana ena a ku Yuda. Mayina awo anali Danieli,+ Hananiya, Misayeli ndi Azariya,+
6 Moredekai anali atatengedwa ku Yerusalemu pamodzi ndi anthu amene anatengedwa kupita ku ukapolo.+ Anthuwa ndi amene anatengedwa pamodzi ndi Yekoniya+ mfumu ya Yuda, amene Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anam’tenga kupita naye ku ukapolo.
2 Pa tsiku lachisanu la mweziwo, m’chaka chachisanu kuchokera pamene Mfumu Yehoyakini anatengedwa ukapolo,+
6 Pakati pa anawo panali ana ena a ku Yuda. Mayina awo anali Danieli,+ Hananiya, Misayeli ndi Azariya,+