Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chotero iye anatengera Yehoyakini+ ku Babulo.+ Anatenga ku Yerusalemu mayi a mfumuyo,+ akazi ake, nduna za panyumba yake,+ ndi akuluakulu a m’dzikolo, n’kuwapititsa ku Babulo.

  • 1 Mbiri 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mwana wa Yehoyakimu anali Yekoniya.+ Yekoniya anabereka Zedekiya.

  • 2 Mbiri 36:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kumayambiriro+ kwa chaka, Mfumu Nebukadinezara inatuma+ asilikali ake omwe anakamutenga n’kubwera naye ku Babulo+ limodzi ndi zinthu zabwinozabwino za m’nyumba ya Yehova.+ Kuwonjezera apo, Nebukadinezara analonga ufumu Zedekiya+ yemwe anali m’bale wa bambo ake kukhala mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu.+

  • Yeremiya 22:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kodi munthu uyu Koniya+ wangokhala chiwiya chonyozeka, chophwanyika+ komanso chosasangalatsa?+ N’chifukwa chiyani iyeyu ndi ana ake akuyenera kugwetsedwa ndi kuponyedwa kudziko limene sakulidziwa?’+

  • Yeremiya 37:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya,+ amene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anamuika kukhala mfumu m’dziko la Yuda,+ anayamba kulamulira m’malo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu.+

  • Yeremiya 52:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako, m’chaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini+ mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 12, pa tsiku la 25 la mweziwo, chaka chimene Evili-merodaki mfumu ya Babulo anakhala mfumu, iye anakomera mtima Yehoyakini mfumu ya Yuda ndi kumutulutsa m’ndende.+

  • Mateyu 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yosiya+ anabereka Yekoniya+ ndi abale ake pa nthawi imene Ayuda anatengedwa kupita ku Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena