Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 31:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndaiwalidwa ngati munthu wakufa amene anthu sakumukumbukiranso.+

      Ndakhala ngati chiwiya chosweka.+

  • Yeremiya 48:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 “‘Anthu akulira pamadenga onse a nyumba za ku Mowabu ndi m’mabwalo ake onse.+ Akulira chifukwa ndaphwanya Mowabu ngati chiwiya chimene sichikundikondweretsa,’+ watero Yehova.

  • Hoseya 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Aisiraeli adzamezedwa+ moti adzakhala pakati pa mitundu ina ya anthu+ ngati chiwiya chosasangalatsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena