Yeremiya 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi munthu uyu Koniya+ wangokhala chiwiya chonyozeka, chophwanyika+ komanso chosasangalatsa?+ N’chifukwa chiyani iyeyu ndi ana ake akuyenera kugwetsedwa ndi kuponyedwa kudziko limene sakulidziwa?’+ Hoseya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Aisiraeli adzamezedwa+ moti adzakhala pakati pa mitundu ina ya anthu+ ngati chiwiya chosasangalatsa.+
28 Kodi munthu uyu Koniya+ wangokhala chiwiya chonyozeka, chophwanyika+ komanso chosasangalatsa?+ N’chifukwa chiyani iyeyu ndi ana ake akuyenera kugwetsedwa ndi kuponyedwa kudziko limene sakulidziwa?’+
8 “Aisiraeli adzamezedwa+ moti adzakhala pakati pa mitundu ina ya anthu+ ngati chiwiya chosasangalatsa.+