11 Pambuyo pake mfumu ya Asuri+ inatenga Aisiraeli n’kupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala,+ ndi ku Habori+ pafupi ndi mtsinje wa Gozani, ndiponso m’mizinda ya Amedi.+
17 “Isiraeli ndi nkhosa yosochera.+ Mikango ndi imene yamuchititsa kuthawa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inadya Isiraeli,+ ndipo ulendo uno Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo yakukuta mafupa ake.+