Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa za pamalo anga odyetsera ziweto!”+ watero Yehova.

  • Yeremiya 50:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu anga akhala ngati gulu la nkhosa zosakazidwa.+ Abusa awo awayendetsa uku ndi uku.+ Awayendetsa uku ndi uku m’mapiri popanda cholinga.+ Awachotsa paphiri ndi chitunda china kupita paphiri ndi chitunda china. Iwo aiwala malo awo ampumulo.+

  • Ezekieli 34:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pang’ono ndi pang’ono zinamwazikana chifukwa chakuti zinalibe m’busa.+ Choncho zinakhala chakudya cha zilombo zonse zakutchire ndipo zinapitiriza kumwazikana.+

  • Mateyu 9:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Poona chikhamu cha anthu, iye anawamvera chisoni,+ chifukwa anali onyukanyuka ndi otayika ngati nkhosa zopanda m’busa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena